Levitiko 13:27 BL92

27 ndipo wansembe amuone tsiku lacisanu ndi ciwiri; ngati cakula pakhungu, wansembe amuche wodetsedwa; ndiyo nthenda yakhate,

Werengani mutu wathunthu Levitiko 13

Onani Levitiko 13:27 nkhani