Levitiko 13:26 BL92

26 Koma akaonapo wansembe, ndipo taonani, mulibe tsitsi loyera m'cikangamo, ndipo sicikumba kubzola khungu, koma cazimba; pamenepo wansembe ambindikiritse masiku asanu ndi awiri;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 13

Onani Levitiko 13:26 nkhani