18 natsitsitize mafuta otsala m'dzanja lace la wansembe, pamutu pa iye wakuti ayeretsedwe; ndipo wansembe amcitire comtetezers pamaso pa Yehova.
Werengani mutu wathunthu Levitiko 14
Onani Levitiko 14:18 nkhani