19 Ndipo wansembe apereke nsembe yaucimo, namcitire comtetezera amene akuti ayeretsedwe, cifukwa ca kudetsedwa kwace; ndipo atatero aphe nsembe yopsereza;
Werengani mutu wathunthu Levitiko 14
Onani Levitiko 14:19 nkhani