20 ndipo wansembe atenthe nsembe yopsereza, ndi nsembe yaufa pa guwa la nsembe; ndipo wansembe amcitire comtetezera, ndipo adzakhala iye woyera.
Werengani mutu wathunthu Levitiko 14
Onani Levitiko 14:20 nkhani