Levitiko 14:30 BL92

30 Ndipo iye apereke imodzi ya njiwazo, kapena limodzi la maunda, monga akhoza kufikana nazo, limodzi la nsembe yaucimo, ndi tina la nsembe yopsereza, pamodzi ndi nsembe yaufa;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 14

Onani Levitiko 14:30 nkhani