47 Ndipo iye wakugona m'nyumbayo atsuke zobvala zace; ndi iye wakudya m'nyumbayo atsuke zobvala zace.
Werengani mutu wathunthu Levitiko 14
Onani Levitiko 14:47 nkhani