48 Ndipo wansembe akalowa, nakaona, ndipo taonani, nthenda siinakula m'nyumba, ataimata nyumba; wansembe aiche nyumbayo yoyera, popeza nthenda yaleka.
Werengani mutu wathunthu Levitiko 14
Onani Levitiko 14:48 nkhani