Levitiko 14:49 BL92

49 Pamenepo atenge mbalame ziwiri, ndi mtengo wamkungudza, ndi ubweya wofiira, ndi hisope, kuti ayeretse nazo nyumbayo;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 14

Onani Levitiko 14:49 nkhani