Levitiko 14:6 BL92

6 natenge nbalame yamoyo, ndi mtengo wankungudza, ndi ubweya wofiira, ndi hisope, nazibviike pamodzi ndi mbalame yamoyo m'mwazi wa mbalame adaipha pamwamba pa madzi oyenda;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 14

Onani Levitiko 14:6 nkhani