Levitiko 14:7 BL92

7 nawaze kasanu ndi kawiri iye amene akuti amyeretse khate lace, namuche woyera, nataye mbalame yamoyo padambo poyera.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 14

Onani Levitiko 14:7 nkhani