Levitiko 15:24 BL92

24 Ndipo ngati mwamuna ali yense agona naye, ndi kudetsa kwace kukhala pa iye, adzakhala wodetsedwa masiku asanu ndi awiri; ndipo kama ali yense agonapo ali wodetsedwa.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 15

Onani Levitiko 15:24 nkhani