7 Ndipo asamapheranso ziwanda nsembe zao, zimene azitsata ndi cigololo. Ili liwakhalire lemba losatha mwa mibadwo yao.
Werengani mutu wathunthu Levitiko 17
Onani Levitiko 17:7 nkhani