Levitiko 18:21 BL92

21 Ndipo usamapereka a mbumba yako kuwapitiriza kumoto cifukwa ca Moleke, usamaipsa dzina la Mulungu wako: Ine ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 18

Onani Levitiko 18:21 nkhani