Levitiko 2:5 BL92

5 Ndipo nsembe yaufa yako ikakhala yokazinga m'ciwaya, ikhale ya ufa wosalala wopanda cotupitsa, wosanganiza ndi mafuta.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 2

Onani Levitiko 2:5 nkhani