Levitiko 2:9 BL92

9 Ndipo wansembeyo atengeko cikumbutso pa nsembe yaufa, nacitenthe pa guwa la nsembe; ndico nsembe yamoto ya pfungo lokoma la kwa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 2

Onani Levitiko 2:9 nkhani