Levitiko 2:8 BL92

8 Ndipo ubwere nayo nsembe yaufa yopangika ndi izi kwa Yehova; ndipo atabwera naco kwa wansembe, iyeyo apite naco ku guwa la nsembe.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 2

Onani Levitiko 2:8 nkhani