Levitiko 20:18 BL92

18 Munthu akagona ndi mkazi ali mumsambo, nakambvula, anabvula kasupe wace, ndi iye mwini anabvula kasupe wa nthenda yace; awadule onse awiri pakati pa anthu a mtundu wao.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 20

Onani Levitiko 20:18 nkhani