Levitiko 20:19 BL92

19 Usamabvula mbale wa mai wako, kapena mlongo wa atate wako; popeza anabvula abale ace; asenze mphulupulu yao.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 20

Onani Levitiko 20:19 nkhani