Levitiko 20:26 BL92

26 Ndipo muzikhala oyera kwa Ine; pakuti Ine Yehova ndine woyera, ndipo ndinakusiyanitsani kwa mitundu ya anthu mukhale anga.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 20

Onani Levitiko 20:26 nkhani