Levitiko 20:27 BL92

27 Munthu wamwamuna kapena wamkazi wakubwebweta, kapena wanyanga, azimupha ndithu; aziwaponya miyala; mwazi wao ukhale pamtu pao.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 20

Onani Levitiko 20:27 nkhani