Levitiko 22:14 BL92

14 Ndipo munthu akadyako cinthu copatulika mosadziwa, azionjezapo limodzi la magawo asanu, nalipereke kwa wansembe, pamodzi ndi copatulikaco.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 22

Onani Levitiko 22:14 nkhani