Levitiko 23:20 BL92

20 Ndi wansembe awaweyule, pamodzi ndi mkate wa zipatso zoyamba, nsembe yoweyula pamaso pa Yehova, pamodzi ndi ana a nkhosa awiriwo; zikhale zopatulikira Yehova, kuti zikhale za wansembe.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 23

Onani Levitiko 23:20 nkhani