Levitiko 23:21 BL92

21 Ndipo mulalikire tsiku lomwelo; kuti mukhale nao msonkhano wopatulika; musamagwira nchito ya masiku ena; ndilo lemba losatha m'nyumba zanu zonse, mwa mibadwo yanu yonse.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 23

Onani Levitiko 23:21 nkhani