Levitiko 24:3 BL92

3 Aroni aikonze kunja kwa nsaru yocinga ya mboni, m'cihema cokomanako, kuyambira madzulo kufikira m'mawa, pamaso pa Yehova nthawi zonse; likhale lemba losatha mwa mibadwo yanu.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 24

Onani Levitiko 24:3 nkhani