Levitiko 25:38 BL92

38 Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakuturutsani m'dziko la Aigupto, kukupatsani dziko la Kanani, kuti ndikhale Mulungu wanu.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 25

Onani Levitiko 25:38 nkhani