Levitiko 26:1 BL92

1 Musamadzipangira mafano, kapena kudziutsira mafano osema, kapena coimiritsa, kapena kuika mwala wozokota m'dziko mwanu kuugwadira umene; popeza Ine ndine Yehova Mulungu wanu.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 26

Onani Levitiko 26:1 nkhani