33 Ndipo ndidzabalalitsa inu mwa amitundu, ndi kusolola lupanga kukutsatani; ndi dziko lanu lidzakhala lopasuka, ndi midzi yanu idzakhala bwinja.
Werengani mutu wathunthu Levitiko 26
Onani Levitiko 26:33 nkhani