Levitiko 26:34 BL92

34 Pamenepo dzikoli lidzakondwera nao masabata ace, masiku onse a kupasuka kwace, pokhala inu m'dziko la adani anu; pamenepo dziko lidzapumula, ndi kukondwera nao masabata ace.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 26

Onani Levitiko 26:34 nkhani