Levitiko 26:41 BL92

41 Inenso ndinayenda motsutsana nao, ndi kuwatengera ku dziko la adani ao. Ngati tsono mtima wao wosadulidwa udzicepetsa, ndipo abvomereza kulanga kwa mphulupulu zao;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 26

Onani Levitiko 26:41 nkhani