Levitiko 26:45 BL92

45 Koma cifukwa ca iwo ndidzawakumbukila pangano la makolo ao, amene ndinawaturutsa m'dziko la Aigupto pamaso pa amitundu, kuti ndikhale Mulungu wao; Ine ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 26

Onani Levitiko 26:45 nkhani