Levitiko 26:8 BL92

8 Asanu ainu adzapitikitsa zana limodzi, ndi zana limodzi la inu adzapitikitsa zikwi khumi; ndi adani anu adzagwa pamaso panu ndi lupanga.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 26

Onani Levitiko 26:8 nkhani