9 Ndipo ndidzatembenukira kwa inu, ndi kukubalitsani, ndi kukucurukitsani; ndipo ndidzakhazika cipangano canga ndinapangana nanuco.
Werengani mutu wathunthu Levitiko 26
Onani Levitiko 26:9 nkhani