Levitiko 27:5 BL92

5 Akakhala munthu wa zaka zisanu kufikira wina wa zaka makumi awiri uwayesere, wamwamuna wa masekeli makumi awiri, ndi wamkazi wa masekeli khumi.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 27

Onani Levitiko 27:5 nkhani