Levitiko 27:6 BL92

6 Akakhala mwana wa mwezi umodzi kufikira zaka zisanu, uziwayesera wamwamuna wa masekeli asanu a siliva, ndi wamkazi wa masekeli atatu a siliva.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 27

Onani Levitiko 27:6 nkhani