Levitiko 3:3 BL92

3 Pamenepo abwere nayo nsembe yamoto ya kwa Yehova, yotengako ku nsembe yoyamika; acotse mafuta akukuta matumbo, ndi mafuta onse akukhala pamatumbo,

Werengani mutu wathunthu Levitiko 3

Onani Levitiko 3:3 nkhani