2 Ndipo aike dzanja lace pa mutu wa copereka cace, ndi kuipha pa cipata ca cihema cokomanako; ndipo ana a Aroni, ansembewo, awaze mwazi wace pa guwa la nsembe pozungulira.
Werengani mutu wathunthu Levitiko 3
Onani Levitiko 3:2 nkhani