Levitiko 4:25 BL92

25 Ndipo wansembe atengeko mwazi wa nsembe yaucimo ndi cala cace, nauike pa nyanga za guwa la nsembe yopsereza, ndi kuthira mwazi wace patsinde pa guwa la nsembe yopsereza.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 4

Onani Levitiko 4:25 nkhani