26 Ndipo atenthe mafuta ace onse pa guwa la nsembe, monga mafuta a nsembe yoyamika; ndipo wansembe amcitire comtetezera, ndipo adzakhululukidwa.
Werengani mutu wathunthu Levitiko 4
Onani Levitiko 4:26 nkhani