1 Ndipo akacimwa munthu, wakuti adamva mau akuwalumbiritsa, ndiye mboni, kapena wakuona, kapena wakudziwa, koma osaulula, azisenza mphulupulu yace;
Werengani mutu wathunthu Levitiko 5
Onani Levitiko 5:1 nkhani