Levitiko 7:14 BL92

14 Ndipo pa zopereka zonsezi atengepo ndi kubwera nako kamtanda kamodzi, kuti kakhale ka nsembe yokweza ya kwa Yehova; kakhale ka wansembe wakuwaza mwazi wa nsembe zoyamika.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 7

Onani Levitiko 7:14 nkhani