Levitiko 7:15 BL92

15 Kunena za nyama ya nsembe volemekeza ya nsembe zoyamika zace, aziidya tsiku lomwelo lakuipereka; asasiyeko kufikira m'mawa.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 7

Onani Levitiko 7:15 nkhani