Levitiko 8:17 BL92

17 Koma ng'ombeyo, ndi cikopa cace, ndi nyama yace, ndi cipwidza cace, anazitentha ndi mote kunja kwa cigono; monga Yehova adamuuza Mose.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 8

Onani Levitiko 8:17 nkhani