Levitiko 8:18 BL92

18 Ndipo anabwera nayo nkhosa yamphongo ya nsembe yopsereza; ndipo Aroni ndi ana ace amuna anaika manja ao pamutu pa mphongoyo.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 8

Onani Levitiko 8:18 nkhani