27 anaika zonsezi m'manja mwa Aroni, ndi m'manja mwa ana ace amuna, naziweyula nsembe yoweyula pamaso pa Yehova.
Werengani mutu wathunthu Levitiko 8
Onani Levitiko 8:27 nkhani