Levitiko 8:28 BL92

28 Pamenepo Mose anazicotsa ku manja ao, nazitentha pa guwa la nsembe, pa nsembe yopsereza; ndizo nsembe zodzaza manja zocita pfungo lokoma; ndiyo nsembe yamoto ya kwa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 8

Onani Levitiko 8:28 nkhani