10 koma mafutawo, ndi imso, ndi cokuta ca mphafa za nsembe yaucimo, anazitentha pa guwa la nsembe; monga Yehova anauza Mose.
Werengani mutu wathunthu Levitiko 9
Onani Levitiko 9:10 nkhani