Levitiko 9:9 BL92

9 Ndipo ana a Aroni anasendera nao mwazi kwa iye; ndipo anabviika cala cace m'mwazimo naupaka pa nyanga za guwa la nsembe, nathira mwaziwo patsinde pa guwa la nsembe;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 9

Onani Levitiko 9:9 nkhani