Levitiko 9:8 BL92

8 Pamenepo Aroni anasendera kufupi kwa guwa la nsembe, napha mwana wa ng'ombe wa nsembe yaucimo, ndiyo ya kwa iye yekha.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 9

Onani Levitiko 9:8 nkhani