Mateyu 1:2 BL92

2 Abrahamu anabala Isake; ndi Isake anabala Yakobo; ndi Yakobo anabala Yuda ndi abale ace;

Werengani mutu wathunthu Mateyu 1

Onani Mateyu 1:2 nkhani